Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1129 Mbuyanga Yesu, ndikapanda Inu
Mbuyanga Yesu, ndikapanda Inu
Ukadza mdima m’mtima mwangamu;
Koma ndinutu dzuwa langa ndithu
Lakuwalitsa m’mtima momwemu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1129 Mbuyanga Yesu, ndikapanda Inu
Mbuyanga Yesu, ndikapanda Inu
Ukadza mdima m’mtima mwangamu;
Koma ndinutu dzuwa langa ndithu
Lakuwalitsa m’mtima momwemu.