Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1116 Kwawo kwa Mbuyako
Kwawo kwa Mbuyako
Udzafikako;
Mwa ulemerero
Udzapuma phee!
Usalowerere,
Mvera Yesuyo,
Ati: “Mwana wanga
Bwera kwathuko.”
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1116 Kwawo kwa Mbuyako
Kwawo kwa Mbuyako
Udzafikako;
Mwa ulemerero
Udzapuma phee!
Usalowerere,
Mvera Yesuyo,
Ati: “Mwana wanga
Bwera kwathuko.”