Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1113 Mtima wa Mbuyako
Mtima wa Mbuyako
Ukukonda ‘we;
Ndiye wakuona
Wopirirabe;
Ukasowa bwenzi,
Usaope ‘yi;
Chikondano chake
Chikwaniradi.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1113 Mtima wa Mbuyako
Mtima wa Mbuyako
Ukukonda ‘we;
Ndiye wakuona
Wopirirabe;
Ukasowa bwenzi,
Usaope ‘yi;
Chikondano chake
Chikwaniradi.