Hymn 1099 Sindidziwatu zamawa, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1099 Sindidziwatu zamawa, Sindidziwatu zamawa, Koma sindiopa; Ndidzakhulupira Inu Kuti mundikonda.