Hymn 1095 Mumtima wakufatsa treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1095 Mumtima wakufatsa Mumtima wakufatsa Akonda kukhalabe; Asankha mtima wakuyera, Ndiwo nyumba yake.