Hymn 1086 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini moyo, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1086 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini moyo, “Khala mwa Ine,” ndinu mwini moyo, Nthambi zouma zidulidwa m’mtengo; Ine wopanda Inu ndifokanso, Zipatso zikasowa msadze ‘ne.