Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1083 “Khala mwa Ine,” Yesu anatero;
“Khala mwa Ine,” Yesu anatero;
Mawu abwino, koma Mbuye wanga
Sin’ngathe ndekha, mukhalitse ine
Mwa ‘Nu ndikhale nawo moyotu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1083 “Khala mwa Ine,” Yesu anatero;
“Khala mwa Ine,” Yesu anatero;
Mawu abwino, koma Mbuye wanga
Sin’ngathe ndekha, mukhalitse ine
Mwa ‘Nu ndikhale nawo moyotu.