Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1082 Ndidzaonana nanu
Ndidzaonana nanu
Mokondwadi.
Oyera mtima onse
Apenya Mbuyeyo.
Kumwamba n’dzaimbira
Kukoma kwanuku;
N’dzatama nthawi zonse
Chikondi chanucho.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1082 Ndidzaonana nanu
Ndidzaonana nanu
Mokondwadi.
Oyera mtima onse
Apenya Mbuyeyo.
Kumwamba n’dzaimbira
Kukoma kwanuku;
N’dzatama nthawi zonse
Chikondi chanucho.