Hymn 1077 Khalatu woyera, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1077 Khalatu woyera, Khalatu woyera, Dziko laipadi; Pemphera kolimba Kwa Yesu Mbuyathu. Yang’anitsa Yesu Ndi kumutsatira, Kuti anthu ena Aonenso Iye.