Hymn 1062 Mkatero ndidzayenda m’njira treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1062 Mkatero ndidzayenda m’njira Mkatero ndidzayenda m’njira Ndi Mulungu wanga, Idzandiunikira nyali Njira ya Kumwamba.