Hymn 1052 Ndilira mtima wotamanda treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1052 Ndilira mtima wotamanda Ndilira mtima wotamanda Mlungu, ndi woyera, E, mtima woyamika mwazi Munandikhetsera.