Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1031 Gwira zintchito zako,
Gwira zintchito zako,
Pomva usiku udza;
Yamba mamawa ndithu
Potuluka dzuwa.
Gwiranso m’nsana monse
Dzuwalo likatentha;
Gwira tsopano ntchito;
Msanga udzaleka.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1031 Gwira zintchito zako,
Gwira zintchito zako,
Pomva usiku udza;
Yamba mamawa ndithu
Potuluka dzuwa.
Gwiranso m’nsana monse
Dzuwalo likatentha;
Gwira tsopano ntchito;
Msanga udzaleka.