Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1016 Mbuye, mwatiuza ‘fe
Mbuye, mwatiuza ‘fe
Tizikhala nyali
Yoonetsa onsewo
Njira yonka kwanu.
Njaliyi ndi ifetu;
Kuunika kwanu
Mutipatse tiwalire
Osokera onse.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1016 Mbuye, mwatiuza ‘fe
Mbuye, mwatiuza ‘fe
Tizikhala nyali
Yoonetsa onsewo
Njira yonka kwanu.
Njaliyi ndi ifetu;
Kuunika kwanu
Mutipatse tiwalire
Osokera onse.