Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1 Ndinu wakuyera!
Ndinu wakuyera!
E, wamphamvu zonse.
Nthawi ya m’mamawayi
Tiimba nyimboyi.
Mlengi wachifundo,
Tikuyamikani,
E! Mlungu Mmodzi
Mwa Atatuwo.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1 Ndinu wakuyera!
Ndinu wakuyera!
E, wamphamvu zonse.
Nthawi ya m’mamawayi
Tiimba nyimboyi.
Mlengi wachifundo,
Tikuyamikani,
E! Mlungu Mmodzi
Mwa Atatuwo.